Yesaya 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho Yehovayo akupatsani chizindikiro anthu inu: Tamverani! Mtsikana+ adzatenga pakati+ ndipo adzabereka mwana wamwamuna.+ Mwanayo adzam’patsa dzina lakuti Emanueli. 1 Akorinto 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti ndikuona ngati Mulungu waika atumwife kukhala ngati omalizira pachionetsero+ monga anthu okaphedwa,+ chifukwa takhala ngati choonetsedwa m’bwalo la masewera+ kudziko, kwa angelo,+ ndi kwa anthu.+
14 Choncho Yehovayo akupatsani chizindikiro anthu inu: Tamverani! Mtsikana+ adzatenga pakati+ ndipo adzabereka mwana wamwamuna.+ Mwanayo adzam’patsa dzina lakuti Emanueli.
9 Pakuti ndikuona ngati Mulungu waika atumwife kukhala ngati omalizira pachionetsero+ monga anthu okaphedwa,+ chifukwa takhala ngati choonetsedwa m’bwalo la masewera+ kudziko, kwa angelo,+ ndi kwa anthu.+