Aefeso 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 chifukwa sitikulimbana+ ndi anthu athupi la magazi ndi nyama ayi, koma ndi maboma,+ maulamuliro,+ olamulira dziko+ a mdimawu, ndi makamu a mizimu yoipa+ m’malo akumwamba. 1 Petulo 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Zinaululidwa kwa iwo kuti sanali kudzitumikira okha,+ koma anali kutumikira inu mwa zinthu zimene tsopano zalengezedwa+ kwa inu. Zimenezi zalengezedwa kwa inu ndi olengeza uthenga wabwino, mwa mzimu woyera+ wotumizidwa kuchokera kumwamba. M’zinthu zimenezi angelo akulakalaka kusuzumiramo.+
12 chifukwa sitikulimbana+ ndi anthu athupi la magazi ndi nyama ayi, koma ndi maboma,+ maulamuliro,+ olamulira dziko+ a mdimawu, ndi makamu a mizimu yoipa+ m’malo akumwamba.
12 Zinaululidwa kwa iwo kuti sanali kudzitumikira okha,+ koma anali kutumikira inu mwa zinthu zimene tsopano zalengezedwa+ kwa inu. Zimenezi zalengezedwa kwa inu ndi olengeza uthenga wabwino, mwa mzimu woyera+ wotumizidwa kuchokera kumwamba. M’zinthu zimenezi angelo akulakalaka kusuzumiramo.+