Salimo 44:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma chifukwa cha inu, tikuphedwa nthawi zonse.Takhala ngati nkhosa zokaphedwa.+ Aroma 8:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Monga mmene Malemba amanenera kuti: “Chifukwa cha inu, tikuphedwa nthawi zonse. Takhala ngati nkhosa zokaphedwa.”+ 2 Akorinto 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 ngati osadziwika koma odziwika bwino,+ ngati oti tikufa koma tikukhalabe ndi moyo,+ ngati olangidwa+ koma osakaphedwa,+ Chivumbulutso 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Atamatula chidindo chachisanu, ndinaona pansi pa guwa lansembe+ pali miyoyo+ ya amene anaphedwa+ chifukwa cha mawu a Mulungu, ndiponso chifukwa cha ntchito yochitira umboni+ imene anali nayo.
36 Monga mmene Malemba amanenera kuti: “Chifukwa cha inu, tikuphedwa nthawi zonse. Takhala ngati nkhosa zokaphedwa.”+
9 ngati osadziwika koma odziwika bwino,+ ngati oti tikufa koma tikukhalabe ndi moyo,+ ngati olangidwa+ koma osakaphedwa,+
9 Atamatula chidindo chachisanu, ndinaona pansi pa guwa lansembe+ pali miyoyo+ ya amene anaphedwa+ chifukwa cha mawu a Mulungu, ndiponso chifukwa cha ntchito yochitira umboni+ imene anali nayo.