Machitidwe 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano ataona mmene Petulo ndi Yohane anali kulankhulira molimba mtima, komanso atazindikira kuti anali anthu osaphunzira ndiponso anthu wamba,+ anadabwa kwambiri. Ndipo anayamba kuwazindikira kuti anali kuyenda ndi Yesu.+ 2 Akorinto 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kulikonse kumene tikupita, timapirira m’matupi mwathu ndipo timakhala pa ngozi yoti tikhoza kuphedwa, ngati mmene Yesu anachitira,+ kuti moyo wa Yesu uonekerenso m’matupi mwathu.+
13 Tsopano ataona mmene Petulo ndi Yohane anali kulankhulira molimba mtima, komanso atazindikira kuti anali anthu osaphunzira ndiponso anthu wamba,+ anadabwa kwambiri. Ndipo anayamba kuwazindikira kuti anali kuyenda ndi Yesu.+
10 Kulikonse kumene tikupita, timapirira m’matupi mwathu ndipo timakhala pa ngozi yoti tikhoza kuphedwa, ngati mmene Yesu anachitira,+ kuti moyo wa Yesu uonekerenso m’matupi mwathu.+