Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Aroma 8:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Pakuti ndatsimikiza mtima kuti imfa, moyo,+ angelo,+ maboma,+ zinthu zimene zilipo, zinthu zimene zikubwera m’tsogolo, mphamvu,+

  • Afilipi 3:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndachita zimenezi kuti ndim’dziwe komanso kuti ndidziwe mphamvu ya kuuka kwake kwa akufa.+ Kutinso ndigawane naye m’masautso+ ake, ndi kulolera kufa imfa monga yake.+

  • 1 Petulo 4:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Koma muzikondwera+ pamene mukugawana nawo masautso a Khristu,+ kuti mukasangalalenso ndi kukondwera kwambiri pa nthawi imene ulemerero wake udzaonekere.*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena