Salimo 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anthu inu, imbani nyimbo motsagana ndi zipangizo zoimbira, kutamanda Yehova amene akukhala m’Ziyoni.+Fotokozani ntchito zake kwa mitundu ya anthu.+ Yesaya 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Fuula mwachisangalalo iwe mkazi wokhala mu Ziyoni, pakuti Woyera wa Isiraeli ndi wamkulu pakati pako.”+ Yesaya 24:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mwezi wathunthu wachita manyazi. Dzuwa lowala lachitanso manyazi,+ pakuti Yehova wa makamu wakhala mfumu+ yaulemerero m’phiri la Ziyoni+ ndi mu Yerusalemu, pamaso pa anthu ake achikulire.+
11 Anthu inu, imbani nyimbo motsagana ndi zipangizo zoimbira, kutamanda Yehova amene akukhala m’Ziyoni.+Fotokozani ntchito zake kwa mitundu ya anthu.+
6 “Fuula mwachisangalalo iwe mkazi wokhala mu Ziyoni, pakuti Woyera wa Isiraeli ndi wamkulu pakati pako.”+
23 Mwezi wathunthu wachita manyazi. Dzuwa lowala lachitanso manyazi,+ pakuti Yehova wa makamu wakhala mfumu+ yaulemerero m’phiri la Ziyoni+ ndi mu Yerusalemu, pamaso pa anthu ake achikulire.+