Yesaya 22:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anthu inu mudzaona ming’alu ya Mzinda wa Davide pakuti idzakhala yambiri,+ ndipo mudzatunga madzi a m’dziwe lakumunsi.+
9 Anthu inu mudzaona ming’alu ya Mzinda wa Davide pakuti idzakhala yambiri,+ ndipo mudzatunga madzi a m’dziwe lakumunsi.+