2 Samueli 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kumeneko atumiki onse a mfumu, Akereti onse ndi Apeleti+ onse, anali kudutsa pamaso pake. Komanso Agiti+ onse, amuna 600 amene anamutsatira* kuchokera ku Gati+ anali kudutsa pamaso pake. 1 Mbiri 18:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Benaya+ mwana wa Yehoyada+ anali mtsogoleri wa Akereti+ ndi Apeleti,+ ndipo ana aamuna a Davide ndiwo anali ndi udindo waukulu kwambiri pamaso pa mfumu.+
18 Kumeneko atumiki onse a mfumu, Akereti onse ndi Apeleti+ onse, anali kudutsa pamaso pake. Komanso Agiti+ onse, amuna 600 amene anamutsatira* kuchokera ku Gati+ anali kudutsa pamaso pake.
17 Benaya+ mwana wa Yehoyada+ anali mtsogoleri wa Akereti+ ndi Apeleti,+ ndipo ana aamuna a Davide ndiwo anali ndi udindo waukulu kwambiri pamaso pa mfumu.+