7 Choncho asilikali a Yowabu,+ Akereti,+ Apeleti+ ndi amuna onse amphamvu anayamba kumuthamangitsa. Iwo anatuluka mu Yerusalemu ndi kuthamangitsa Sheba mwana wa Bikiri.
17 Benaya+ mwana wa Yehoyada+ anali mtsogoleri wa Akereti+ ndi Apeleti,+ ndipo ana aamuna a Davide ndiwo anali ndi udindo waukulu kwambiri pamaso pa mfumu.+