2 Samueli 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kumeneko atumiki onse a mfumu, Akereti onse ndi Apeleti+ onse, anali kudutsa pamaso pake. Komanso Agiti+ onse, amuna 600 amene anamutsatira* kuchokera ku Gati+ anali kudutsa pamaso pake. 1 Mafumu 1:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Wansembe Zadoki,+ mneneri Natani,+ Benaya+ mwana wa Yehoyada, Akereti+ ndi Apeleti+ anatsetsereka n’kukakweza Solomo panyulu yaikazi ya Mfumu Davide,+ kenako anapita naye ku Gihoni.+
18 Kumeneko atumiki onse a mfumu, Akereti onse ndi Apeleti+ onse, anali kudutsa pamaso pake. Komanso Agiti+ onse, amuna 600 amene anamutsatira* kuchokera ku Gati+ anali kudutsa pamaso pake.
38 Wansembe Zadoki,+ mneneri Natani,+ Benaya+ mwana wa Yehoyada, Akereti+ ndi Apeleti+ anatsetsereka n’kukakweza Solomo panyulu yaikazi ya Mfumu Davide,+ kenako anapita naye ku Gihoni.+