1 Samueli 27:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Patapita nthawi, uthenga unafika kwa Sauli wonena kuti Davide anathawira ku Gati. Atamva zimenezo sanapitenso kukam’sakasaka.+ 1 Mbiri 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pambuyo pake, Davide anapha Afilisiti+ ndi kuwagonjetsa, ndipo anawalanda mzinda wa Gati+ ndi midzi yake yozungulira.
4 Patapita nthawi, uthenga unafika kwa Sauli wonena kuti Davide anathawira ku Gati. Atamva zimenezo sanapitenso kukam’sakasaka.+
18 Pambuyo pake, Davide anapha Afilisiti+ ndi kuwagonjetsa, ndipo anawalanda mzinda wa Gati+ ndi midzi yake yozungulira.