2 Samueli 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho asilikali a Yowabu,+ Akereti, Apeleti+ ndi amuna onse amphamvu anayamba kumusakasaka. Iwo anachoka ku Yerusalemu nʼkupita kukafunafuna Sheba mwana wa Bikiri.
7 Choncho asilikali a Yowabu,+ Akereti, Apeleti+ ndi amuna onse amphamvu anayamba kumusakasaka. Iwo anachoka ku Yerusalemu nʼkupita kukafunafuna Sheba mwana wa Bikiri.