1 Mafumu 1:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Wansembe Zadoki,+ mneneri Natani,+ Benaya+ mwana wa Yehoyada, Akereti+ ndi Apeleti+ anatsetsereka n’kukakweza Solomo panyulu yaikazi ya Mfumu Davide,+ kenako anapita naye ku Gihoni.+
38 Wansembe Zadoki,+ mneneri Natani,+ Benaya+ mwana wa Yehoyada, Akereti+ ndi Apeleti+ anatsetsereka n’kukakweza Solomo panyulu yaikazi ya Mfumu Davide,+ kenako anapita naye ku Gihoni.+