14 Ndife amene tinakaukira kum’mwera kwa dziko la Akereti+ ndi dera la Yuda komanso kum’mwera kwa dera la Kalebe.+ Ndipo mzinda wa Zikilaga tinautentha ndi moto.”
5 “Tsoka kwa anthu okhala m’chigawo cha m’mphepete mwa nyanja, mtundu wa Akereti.+ Yehova wakudzudzulani anthu inu. Iwe Kanani, dziko la Afilisiti, nawenso ndidzakuwononga, kotero kuti m’dziko lako simudzatsala munthu aliyense.+