2 Mafumu 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anthuwo atamva zimenezi, msangamsanga aliyense anavula malaya ake+ n’kumuyalira pamasitepe popanda kanthu. Kenako anayamba kuliza malipenga,+ ndipo anali kunena kuti: “Yehu wakhala mfumu!”+ Mateyu 21:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo anabweretsa bulu uja limodzi ndi mwana wake wamphongo. Kenako anayala malaya awo akunja pa abuluwo ndipo iye anakwerapo.+ Maliko 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho anabweretsa bulu+ uja kwa Yesu. Kenako anayala malaya awo akunja pabuluyo, ndipo iye anakwerapo.+ Yohane 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma pamene Yesu anapeza bulu wamng’ono,+ anakwera pa iye monga mmene Malemba amanenera kuti:
13 Anthuwo atamva zimenezi, msangamsanga aliyense anavula malaya ake+ n’kumuyalira pamasitepe popanda kanthu. Kenako anayamba kuliza malipenga,+ ndipo anali kunena kuti: “Yehu wakhala mfumu!”+
7 Iwo anabweretsa bulu uja limodzi ndi mwana wake wamphongo. Kenako anayala malaya awo akunja pa abuluwo ndipo iye anakwerapo.+
7 Choncho anabweretsa bulu+ uja kwa Yesu. Kenako anayala malaya awo akunja pabuluyo, ndipo iye anakwerapo.+