1 Mafumu 1:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Wansembe Zadoki,+ mneneri Natani,+ Benaya+ mwana wa Yehoyada, Akereti+ ndi Apeleti+ anatsetsereka n’kukakweza Solomo panyulu yaikazi ya Mfumu Davide,+ kenako anapita naye ku Gihoni.+ Luka 19:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Pamenepo iwo anamutenga ndi kupita naye kwa Yesu. Kenako iwo anaponya malaya awo akunja pabuluyo ndi kukwezapo Yesu.+ Yohane 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma pamene Yesu anapeza bulu wamng’ono,+ anakwera pa iye monga mmene Malemba amanenera kuti:
38 Wansembe Zadoki,+ mneneri Natani,+ Benaya+ mwana wa Yehoyada, Akereti+ ndi Apeleti+ anatsetsereka n’kukakweza Solomo panyulu yaikazi ya Mfumu Davide,+ kenako anapita naye ku Gihoni.+
35 Pamenepo iwo anamutenga ndi kupita naye kwa Yesu. Kenako iwo anaponya malaya awo akunja pabuluyo ndi kukwezapo Yesu.+