Luka 19:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Pamenepo iwo anamutenga nʼkupita naye kwa Yesu. Kenako iwo anaponya malaya awo akunja pabuluyo ndipo Yesu anakwerapo.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:35 Yesu—Ndi Njira, tsa. 238 Nsanja ya Olonda,11/1/1989, tsa. 8
35 Pamenepo iwo anamutenga nʼkupita naye kwa Yesu. Kenako iwo anaponya malaya awo akunja pabuluyo ndipo Yesu anakwerapo.+