Mateyu 21:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo anabweretsa bulu uja limodzi ndi mwana wake wamphongo. Kenako anayala malaya awo akunja pa abuluwo ndipo iye anakwerapo.+ Yohane 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma pamene Yesu anapeza bulu wamng’ono,+ anakwera pa iye monga mmene Malemba amanenera kuti:
7 Iwo anabweretsa bulu uja limodzi ndi mwana wake wamphongo. Kenako anayala malaya awo akunja pa abuluwo ndipo iye anakwerapo.+