1 Mbiri 18:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Benaya+ mwana wa Yehoyada+ anali mtsogoleri wa Akereti+ ndi Apeleti,+ ndipo ana aamuna a Davide ndiwo anali ndi udindo waukulu kwambiri pamaso pa mfumu.+
17 Benaya+ mwana wa Yehoyada+ anali mtsogoleri wa Akereti+ ndi Apeleti,+ ndipo ana aamuna a Davide ndiwo anali ndi udindo waukulu kwambiri pamaso pa mfumu.+