1 Mafumu 2:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Itatero, mfumuyo inalamula Benaya mwana wa Yehoyada amene ananyamuka n’kukakantha Simeyi, ndipo anafa.+ Choncho ufumuwo unakhazikika m’manja mwa Solomo.+
46 Itatero, mfumuyo inalamula Benaya mwana wa Yehoyada amene ananyamuka n’kukakantha Simeyi, ndipo anafa.+ Choncho ufumuwo unakhazikika m’manja mwa Solomo.+