1 Mafumu 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Solomo anakhala pampando wachifumu wa Davide bambo ake,+ ndipo m’kupita kwa nthawi, ufumu wake unakhazikika.+ 2 Mbiri 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Solomo mwana wa Davide anapitiriza kukhala wamphamvu mu ufumu wake.+ Yehova Mulungu wake anali naye,+ ndipo anapitiriza kumukulitsa kuposa wina aliyense.+ Miyambo 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kuchita zinthu zoipa kumanyansa mafumu,+ chifukwa mpando wachifumu umakhazikika ndi chilungamo.+ Miyambo 29:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pochita zinthu zachilungamo, mfumu imachititsa dziko kulimba,+ koma munthu wokonda ziphuphu amaligwetsa.+
12 Solomo anakhala pampando wachifumu wa Davide bambo ake,+ ndipo m’kupita kwa nthawi, ufumu wake unakhazikika.+
1 Solomo mwana wa Davide anapitiriza kukhala wamphamvu mu ufumu wake.+ Yehova Mulungu wake anali naye,+ ndipo anapitiriza kumukulitsa kuposa wina aliyense.+
4 Pochita zinthu zachilungamo, mfumu imachititsa dziko kulimba,+ koma munthu wokonda ziphuphu amaligwetsa.+