Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 18:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 M’chaka cha 14 cha Mfumu Hezekiya, Senakeribu+ mfumu ya Asuri+ anabwera kudzachita nkhondo ndi mizinda yonse ya Ayuda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri, ndipo analanda mizindayo.

  • 2 Mbiri 36:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Iyo inatentha nyumba ya Mulungu woona+ ndi kugwetsa mpanda+ wa Yerusalemu. Ababulowo anatenthanso ndi moto nyumba zonse zokhala ndi mipanda yolimba kwambiri za mzindawo ndi zinthu zake zonse zabwinozabwino,+ mpaka zonse zinawonongedwa.+

  • Yeremiya 17:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 “‘“Koma ngati simudzamvera mawu anga akuti muziona tsiku la sabata kukhala lopatulika ndi kuti musamanyamule katundu+ kulowa naye pazipata za Yerusalemu pa tsiku la sabata, ine ndidzatentha ndi moto zipata za mzindawu.+ Motowo udzanyeketsa nsanja zokhalamo za Yerusalemu+ ndipo sudzazimitsidwa.”’”+

  • Yeremiya 34:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Anamuuza mawu amenewa pamene magulu ankhondo a mfumu ya Babulo anali kumenyana ndi Yerusalemu ndi mizinda ina yonse ya mu Yuda,+ kuphatikizapo Lakisi+ ndi Azeka.+ Mizinda imeneyi inali ndi mipanda yolimba kwambiri+ ndipo ndi imene inali isanawonongedwe pamizinda ya mu Yuda.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena