2 Mbiri 27:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 M’dera lamapiri la Yuda+ anamangamo mizinda+ ndipo m’dera lankhalango+ anamangamo malo okhala ndi mipanda yolimba kwambiri+ ndiponso nsanja.+
4 M’dera lamapiri la Yuda+ anamangamo mizinda+ ndipo m’dera lankhalango+ anamangamo malo okhala ndi mipanda yolimba kwambiri+ ndiponso nsanja.+