2 Mbiri 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Zinthu zinapitiriza kumuyendera bwino Yehosafati ndipo mphamvu zake zinapitiriza kukula kwambiri.+ Iye anayamba kumanga m’dziko la Yuda malo okhala ndi mipanda yolimba kwambiri,+ ndiponso mizinda yosungirako zinthu.+
12 Zinthu zinapitiriza kumuyendera bwino Yehosafati ndipo mphamvu zake zinapitiriza kukula kwambiri.+ Iye anayamba kumanga m’dziko la Yuda malo okhala ndi mipanda yolimba kwambiri,+ ndiponso mizinda yosungirako zinthu.+