1 Samueli 23:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Davide anapitiriza kukhala mwamantha chifukwa Sauli anali kufunafuna moyo wake, pamene Davideyo anali m’chipululu cha Zifi ku Horesi.*+
15 Davide anapitiriza kukhala mwamantha chifukwa Sauli anali kufunafuna moyo wake, pamene Davideyo anali m’chipululu cha Zifi ku Horesi.*+