-
Yoswa 14:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Choncho, ndipatseni dera lamapiri ili limene Yehova anandilonjeza pa tsiku lija.+ Pa tsikulo, ngakhale inuyo munamva kuti kumeneko kuli Aanaki+ ndi mizinda ikuluikulu yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri.+ Koma mosakayikira Yehova akakhala nane,+ ndipo ndikawapitikitsa ndithu monga mmene Yehova analonjezera.”+
-