Yoswa 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chotero Mose anandilumbirira tsiku limenelo kuti, ‘Dziko limene wakaliponda ndi mapazi ako+ lidzakhala cholowa chako ndi cha ana ako mpaka kalekale, chifukwa watsatira Yehova Mulungu wanga ndi mtima wako wonse.’+
9 Chotero Mose anandilumbirira tsiku limenelo kuti, ‘Dziko limene wakaliponda ndi mapazi ako+ lidzakhala cholowa chako ndi cha ana ako mpaka kalekale, chifukwa watsatira Yehova Mulungu wanga ndi mtima wako wonse.’+