Salimo 101:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Maso anga ali pa okhulupirika a padziko lapansi,+Kuti akhale ndi ine.+Woyenda m’njira yowongoka,+Ndi amene adzanditumikira.+ Miyambo 28:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Munthu wochita zinthu mokhulupirika adzapeza madalitso ambiri,+ koma woyesetsa kuti apeze chuma mofulumira, sadzapitiriza kukhala wosalakwa.+
6 Maso anga ali pa okhulupirika a padziko lapansi,+Kuti akhale ndi ine.+Woyenda m’njira yowongoka,+Ndi amene adzanditumikira.+
20 Munthu wochita zinthu mokhulupirika adzapeza madalitso ambiri,+ koma woyesetsa kuti apeze chuma mofulumira, sadzapitiriza kukhala wosalakwa.+