Numeri 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova akatikomera mtima,+ ndithu adzatilowetsa m’dzikolo n’kulipereka kwa ife, dziko loyenda mkaka ndi uchi.+ Salimo 60:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndi thandizo la Mulungu, tidzalandira mphamvu,+Ndipo Mulungu adzapondereza adani athu.+ Aroma 8:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiye tinene kuti chiyani pa zinthu zimenezi? Ngati Mulungu ali kumbali yathu, ndani adzatsutsana nafe?+ Afilipi 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pa zinthu zonse, ndimapeza mphamvu kuchokera kwa iye amene amandipatsa mphamvu.+
8 Yehova akatikomera mtima,+ ndithu adzatilowetsa m’dzikolo n’kulipereka kwa ife, dziko loyenda mkaka ndi uchi.+
31 Ndiye tinene kuti chiyani pa zinthu zimenezi? Ngati Mulungu ali kumbali yathu, ndani adzatsutsana nafe?+