Yoswa 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho Kalebe anapitikitsa ana atatu a Anaki+ kuderalo. Anawo anali Sesai,+ Ahimani, ndi Talimai,+ obadwa kwa Anaki.+ Oweruza 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Atapereka Heburoni kwa Kalebe monga mmene Mose analonjezera,+ Kalebe anapitikitsa ana atatu aamuna a Anaki amene anali kukhala mmenemo.+
14 Choncho Kalebe anapitikitsa ana atatu a Anaki+ kuderalo. Anawo anali Sesai,+ Ahimani, ndi Talimai,+ obadwa kwa Anaki.+
20 Atapereka Heburoni kwa Kalebe monga mmene Mose analonjezera,+ Kalebe anapitikitsa ana atatu aamuna a Anaki amene anali kukhala mmenemo.+