Oweruza 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Motero fuko la Yuda linapita kukamenyana ndi Akanani amene anali kukhala ku Heburoni,+ (poyamba dzina la mzinda wa Heburoni linali Kiriyati-ariba).+ Iwo anapha Sesai, Ahimani ndi Talimai.+
10 Motero fuko la Yuda linapita kukamenyana ndi Akanani amene anali kukhala ku Heburoni,+ (poyamba dzina la mzinda wa Heburoni linali Kiriyati-ariba).+ Iwo anapha Sesai, Ahimani ndi Talimai.+