Yoswa 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho Kalebe anathamangitsa mbadwa za ana atatu a Anaki+ kuderalo. Anawo anali Sesai, Ahimani ndi Talimai.+
14 Choncho Kalebe anathamangitsa mbadwa za ana atatu a Anaki+ kuderalo. Anawo anali Sesai, Ahimani ndi Talimai.+