Yeremiya 34:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 pamene asilikali a mfumu ya Babulo ankamenyana ndi Yerusalemu komanso mizinda yonse ya mu Yuda imene inatsala,+ kuphatikizapo Lakisi+ ndi Azeka.+ Imeneyi ndi mizinda yokhayo ya mipanda yolimba kwambiri imene inatsala mu Yuda. Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 34:7 Nsanja ya Olonda,11/15/2007, tsa. 14
7 pamene asilikali a mfumu ya Babulo ankamenyana ndi Yerusalemu komanso mizinda yonse ya mu Yuda imene inatsala,+ kuphatikizapo Lakisi+ ndi Azeka.+ Imeneyi ndi mizinda yokhayo ya mipanda yolimba kwambiri imene inatsala mu Yuda.