Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 32:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Milungu imene inali kudya mafuta a nsembe zawo,+

      Ndi kumwa vinyo wa nsembe zawo zachakumwa?+

      Ibwere kudzakuthandizani.+

      Ikhaletu malo anu obisalamo.+

  • Yesaya 28:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Pakuti anthu inu mwanena kuti: “Ife tachita pangano ndi Imfa.+ Taona masomphenya limodzi ndi Manda.+ Ngati madzi osefukira atadutsa kuno, safika kwa ife pakuti bodza talisandutsa pothawirapo pathu,+ ndiponso tabisala m’chinyengo.”+

  • Yeremiya 10:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Munthu aliyense wachita zinthu mopanda nzeru kwambiri moti ndi zoonekeratu kuti sakudziwa kalikonse.+ Mmisiri wa zitsulo aliyense adzachita manyazi chifukwa cha chifaniziro chake chosula.+ Pakuti chifaniziro chake chopangidwa ndi chitsulo chosungunula ndi mulungu wonama+ ndipo mafano amenewa alibe moyo.+

  • Habakuku 2:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Kodi chifaniziro chosema, chifaniziro chopangidwa ndi chitsulo chosungunula ndiponso mphunzitsi wonama,+ zili ndi phindu lanji+ kuti wozipanga azizikhulupirira+ ndipo azipanga milungu yopanda pake yosalankhula?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena