Salimo 97:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Onse amene akupembedza chifaniziro chilichonse achite manyazi.+Amene amadzitama chifukwa cha milungu yopanda pake achite manyazi.+Muweramireni, inu milungu yonse.+ Yesaya 42:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anthu amene akudalira zifaniziro zosema, amene akuuza zifaniziro zopangidwa ndi chitsulo chosungunula kuti: “Ndinu milungu yathu,” adzathawa ndipo adzachita manyazi kwambiri.+ Yesaya 44:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anzake onse adzachita manyazi,+ ndipotu amisiriwo ndi anthu ochokera kufumbi. Onsewo adzasonkhana pamodzi.+ Adzaima chilili. Adzachita mantha. Onsewo adzachitira limodzi manyazi.+
7 Onse amene akupembedza chifaniziro chilichonse achite manyazi.+Amene amadzitama chifukwa cha milungu yopanda pake achite manyazi.+Muweramireni, inu milungu yonse.+
17 Anthu amene akudalira zifaniziro zosema, amene akuuza zifaniziro zopangidwa ndi chitsulo chosungunula kuti: “Ndinu milungu yathu,” adzathawa ndipo adzachita manyazi kwambiri.+
11 Anzake onse adzachita manyazi,+ ndipotu amisiriwo ndi anthu ochokera kufumbi. Onsewo adzasonkhana pamodzi.+ Adzaima chilili. Adzachita mantha. Onsewo adzachitira limodzi manyazi.+