1 Samueli 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsiku lotsatira Aasidodi anadzuka m’mawa kwambiri, ndipo anapeza Dagoni atagwa pansi chafufumimba patsogolo pa likasa la Yehova.+ Zitatero, anatenga Dagoni ndi kumubwezeretsa pamalo ake.+ 1 Samueli 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu a ku Asidodi ataona kuti zafika pamenepo, anati: “Musalole kuti likasa la Mulungu wa Isiraeli likhale ndi ife kuno, chifukwa dzanja lake latisautsa kwambiri pamodzi ndi Dagoni mulungu wathu.”+ Yesaya 1:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pakuti anthu adzachita manyazi ndi mitengo ikuluikulu imene inu munali kuilakalaka,+ ndipo mudzagwetsa nkhope zanu chifukwa cha minda imene mwasankha.+
3 Tsiku lotsatira Aasidodi anadzuka m’mawa kwambiri, ndipo anapeza Dagoni atagwa pansi chafufumimba patsogolo pa likasa la Yehova.+ Zitatero, anatenga Dagoni ndi kumubwezeretsa pamalo ake.+
7 Anthu a ku Asidodi ataona kuti zafika pamenepo, anati: “Musalole kuti likasa la Mulungu wa Isiraeli likhale ndi ife kuno, chifukwa dzanja lake latisautsa kwambiri pamodzi ndi Dagoni mulungu wathu.”+
29 Pakuti anthu adzachita manyazi ndi mitengo ikuluikulu imene inu munali kuilakalaka,+ ndipo mudzagwetsa nkhope zanu chifukwa cha minda imene mwasankha.+