Yesaya 41:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Aliyense anali kuthandiza mnzake, ndipo munthu anali kuuza mbale wake kuti: “Limba mtima.”+