1 Samueli 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Limbani mtima ndi kuchita chamuna Afilisitinu, kuti musatumikire Aheberi ngati mmene iwo akutumikirirani.+ Chitani chamuna ndi kumenya nkhondo!” Yoweli 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Sulani makasu anu a pulawo kuti akhale malupanga, ndiponso zida zanu zosadzira mitengo+ kuti zikhale mikondo ing’onoing’ono. Munthu wofooka anene kuti: “Ndine mwamuna wamphamvu.”+
9 Limbani mtima ndi kuchita chamuna Afilisitinu, kuti musatumikire Aheberi ngati mmene iwo akutumikirirani.+ Chitani chamuna ndi kumenya nkhondo!”
10 Sulani makasu anu a pulawo kuti akhale malupanga, ndiponso zida zanu zosadzira mitengo+ kuti zikhale mikondo ing’onoing’ono. Munthu wofooka anene kuti: “Ndine mwamuna wamphamvu.”+