Yesaya 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Waiwala Mulungu+ amene amakupulumutsa,Ndipo walephera kukumbukira Thanthwe+ limene limakuteteza. Nʼchifukwa chake ukulima minda yokongola*Nʼkudzalamo mphukira ya mlendo.* Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:10 Yesaya 1, ptsa. 196-197
10 Waiwala Mulungu+ amene amakupulumutsa,Ndipo walephera kukumbukira Thanthwe+ limene limakuteteza. Nʼchifukwa chake ukulima minda yokongola*Nʼkudzalamo mphukira ya mlendo.*