Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 16:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Nenani kuti: ‘Tipulumutseni, inu Mulungu wachipulumutso chathu,+

      Tisonkhanitseni pamodzi ndi kutilanditsa kwa anthu a mitundu ina,+

      Kuti titamande dzina lanu loyera,+ ndiponso kuti tilankhule mokondwa pokutamandani.+

  • Salimo 65:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Mudzatiyankha ndi zinthu zochititsa mantha zochitika mwachilungamo,+

      Inu Mulungu wa chipulumutso chathu,+

      Inu Chidaliro cha malire onse a dziko lapansi ndi anthu okhala pafupi ndi nyanja zakutali.+

  • Salimo 79:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Tithandizeni inu Mulungu wa chipulumutso chathu,+

      Kuti dzina lanu lilemekezedwe.+

      Tipulumutseni ndi kutikhululukira* machimo athu chifukwa cha dzina lanu.+

  • Habakuku 3:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Ine ndidzakondwerabe mwa Yehova+ ndipo ndidzasangalala mwa Mulungu wachipulumutso changa.+

  • Chivumbulutso 7:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Iwo anapitirizabe kufuula ndi mawu okweza, kuti: “Chipulumutso chathu chachokera kwa Mulungu wathu,+ amene wakhala pampando wachifumu,+ ndi kwa Mwanawankhosa.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena