Salimo 149:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 149 Tamandani Ya, anthu inu!+Imbirani Yehova nyimbo yatsopano,+Muimbireni nyimbo zomutamanda mu mpingo wa anthu ake okhulupirika.+ Yesaya 43:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 ndiponso kuti anthu amene ndinawapanga kuti akhale anga, anene za ulemerero wanga.+ Akolose 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mawu a Khristu akhazikike mwa inu ndipo akupatseni nzeru zonse.+ Pitirizani kuphunzitsana+ ndi kulangizana mwa masalimo,+ nyimbo zotamanda Mulungu, ndi nyimbo zauzimu+ zogwira mtima. Pitirizani kuimbira Yehova+ m’mitima yanu.
149 Tamandani Ya, anthu inu!+Imbirani Yehova nyimbo yatsopano,+Muimbireni nyimbo zomutamanda mu mpingo wa anthu ake okhulupirika.+
16 Mawu a Khristu akhazikike mwa inu ndipo akupatseni nzeru zonse.+ Pitirizani kuphunzitsana+ ndi kulangizana mwa masalimo,+ nyimbo zotamanda Mulungu, ndi nyimbo zauzimu+ zogwira mtima. Pitirizani kuimbira Yehova+ m’mitima yanu.