Akolose 1:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Tikulengeza,+ kuchenjeza, ndi kuphunzitsa munthu aliyense za ameneyu mu nzeru zonse,+ kuti tipereke munthu aliyense kwa Mulungu ali wokhwima mwauzimu+ mogwirizana ndi Khristu. Tito 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma iwe pitiriza kulankhula zinthu zogwirizana ndi chiphunzitso cholondola.+
28 Tikulengeza,+ kuchenjeza, ndi kuphunzitsa munthu aliyense za ameneyu mu nzeru zonse,+ kuti tipereke munthu aliyense kwa Mulungu ali wokhwima mwauzimu+ mogwirizana ndi Khristu.