Salimo 113:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 113 Tamandani Ya, anthu inu!+Inu atumiki a Yehova, mutamandeni,+Tamandani dzina la Yehova.+