Salimo 33:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Fuulani mosangalala chifukwa cha Yehova, inu nonse olungama.+M’poyenera kuti owongoka mtima atamande Mulungu.+ Salimo 103:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tamandani Yehova inu makamu ake onse,+Inu atumiki ake onse ochita chifuniro chake.+ Aefeso 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mukakhala pakati panu muziimba masalimo,+ nyimbo zotamanda+ Mulungu, ndiponso nyimbo zauzimu. Muziimba+ nyimbo zotamanda+ Yehova m’mitima mwanu, Chivumbulutso 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Komanso, kunamveka mawu ochokera kumpando wachifumu akuti: “Muzitamanda Mulungu wathu, inu nonse akapolo+ ake, inu omuopa, olemekezeka ndi onyozeka omwe.”+
33 Fuulani mosangalala chifukwa cha Yehova, inu nonse olungama.+M’poyenera kuti owongoka mtima atamande Mulungu.+
19 Mukakhala pakati panu muziimba masalimo,+ nyimbo zotamanda+ Mulungu, ndiponso nyimbo zauzimu. Muziimba+ nyimbo zotamanda+ Yehova m’mitima mwanu,
5 Komanso, kunamveka mawu ochokera kumpando wachifumu akuti: “Muzitamanda Mulungu wathu, inu nonse akapolo+ ake, inu omuopa, olemekezeka ndi onyozeka omwe.”+