1 Mafumu 22:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mikaya anapitiriza kunena kuti: “Choncho imvani mawu a Yehova:+ Ndinaona Yehova atakhala pampando wake wachifumu,+ makamu onse akumwamba ataimirira kudzanja lake lamanja ndi kumanzere kwake.+ Salimo 148:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mutamandeni, inu angelo ake onse.+Mutamandeni, inu khamu lake lonse.+ Yesaya 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Choncho mawu a Ambuye woona, Yehova wa makamu, Wamphamvu wa Isiraeli,+ ndi akuti: “Eya! Ndidzibweretsera mpumulo pochotsa adani anga ndipo ndibwezera+ odana nane.+ Luka 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mwadzidzidzi, panaoneka khamu lalikulu lakumwamba+ pamodzi ndi mngeloyo, likutamanda Mulungu+ kuti:
19 Mikaya anapitiriza kunena kuti: “Choncho imvani mawu a Yehova:+ Ndinaona Yehova atakhala pampando wake wachifumu,+ makamu onse akumwamba ataimirira kudzanja lake lamanja ndi kumanzere kwake.+
24 Choncho mawu a Ambuye woona, Yehova wa makamu, Wamphamvu wa Isiraeli,+ ndi akuti: “Eya! Ndidzibweretsera mpumulo pochotsa adani anga ndipo ndibwezera+ odana nane.+
13 Mwadzidzidzi, panaoneka khamu lalikulu lakumwamba+ pamodzi ndi mngeloyo, likutamanda Mulungu+ kuti: