Mateyu 13:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Mwana wa munthu adzatumiza angelo ake, ndipo adzachotsa mu ufumu wake zinthu zonse zopunthwitsa+ ndiponso anthu osamvera malamulo. Aheberi 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiponso ponena za angelo, iye akuti: “Amapanga angelo ake kukhala mizimu, ndipo amapanganso antchito ake otumikira ena kukhala lawi la moto.”+
41 Mwana wa munthu adzatumiza angelo ake, ndipo adzachotsa mu ufumu wake zinthu zonse zopunthwitsa+ ndiponso anthu osamvera malamulo.
7 Ndiponso ponena za angelo, iye akuti: “Amapanga angelo ake kukhala mizimu, ndipo amapanganso antchito ake otumikira ena kukhala lawi la moto.”+