Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 33:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Muimbireni nyimbo yatsopano.+

      Muimbireni choimbira cha zingwe ndi mtima wonse ndi kufuula mosangalala.+

  • Salimo 96:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 96 Imbirani Yehova nyimbo yatsopano.+

      Imbirani Yehova, inu anthu nonse okhala padziko lapansi.+

  • Yesaya 42:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Imbirani Yehova nyimbo yatsopano.+ M’tamandeni kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+ M’tamandeni inu amuna amene mumadalira nyanja+ ndi zonse zokhala mmenemo, ndiponso inu zilumba ndi anthu okhala m’zilumbazo.+

  • Chivumbulutso 5:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Iwo anali kuimba nyimbo yatsopano,+ yakuti: “Inu ndinu woyenera kutenga mpukutuwo ndi kumatula zidindo zake zomatira, chifukwa munaphedwa, ndipo ndi magazi anu,+ munagula+ anthu kuti atumikire Mulungu.+ Anthu ochokera mu fuko lililonse, chinenero chilichonse, mtundu uliwonse, ndi dziko lililonse.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena