1 Mbiri 16:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Imbirani Yehova, inu nonse okhala padziko lapansi!+Tsiku ndi tsiku lengezani chipulumutso chimene amapereka!+ Salimo 33:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Muimbireni nyimbo yatsopano.+Muimbireni choimbira cha zingwe ndi mtima wonse ndi kufuula mosangalala.+ Salimo 40:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Komanso anaika mawu a nyimbo yatsopano m’kamwa mwanga,Nyimbo yotamanda Mulungu wathu.+Ambiri adzaona zimenezi ndipo adzachita mantha,+Iwo adzakhulupirira Yehova.+ Salimo 98:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 98 IMBIRANI Yehova nyimbo yatsopano,+Pakuti zimene wachita ndi zodabwitsa.+Dzanja lake lamanja, ndithu mkono wake woyera, wabweretsa chipulumutso.+ Salimo 149:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 149 Tamandani Ya, anthu inu!+Imbirani Yehova nyimbo yatsopano,+Muimbireni nyimbo zomutamanda mu mpingo wa anthu ake okhulupirika.+ Yesaya 42:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Imbirani Yehova nyimbo yatsopano.+ M’tamandeni kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+ M’tamandeni inu amuna amene mumadalira nyanja+ ndi zonse zokhala mmenemo, ndiponso inu zilumba ndi anthu okhala m’zilumbazo.+
23 Imbirani Yehova, inu nonse okhala padziko lapansi!+Tsiku ndi tsiku lengezani chipulumutso chimene amapereka!+
3 Muimbireni nyimbo yatsopano.+Muimbireni choimbira cha zingwe ndi mtima wonse ndi kufuula mosangalala.+
3 Komanso anaika mawu a nyimbo yatsopano m’kamwa mwanga,Nyimbo yotamanda Mulungu wathu.+Ambiri adzaona zimenezi ndipo adzachita mantha,+Iwo adzakhulupirira Yehova.+
98 IMBIRANI Yehova nyimbo yatsopano,+Pakuti zimene wachita ndi zodabwitsa.+Dzanja lake lamanja, ndithu mkono wake woyera, wabweretsa chipulumutso.+
149 Tamandani Ya, anthu inu!+Imbirani Yehova nyimbo yatsopano,+Muimbireni nyimbo zomutamanda mu mpingo wa anthu ake okhulupirika.+
10 Imbirani Yehova nyimbo yatsopano.+ M’tamandeni kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+ M’tamandeni inu amuna amene mumadalira nyanja+ ndi zonse zokhala mmenemo, ndiponso inu zilumba ndi anthu okhala m’zilumbazo.+