Salimo 40:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chilungamo chanu sindinachibise mumtima mwanga.+Ndinalengeza za kukhulupirika kwanu ndi chipulumutso chanu.+Sindinabise kukoma mtima kwanu kosatha ndi choonadi chanu mumpingo waukulu.”+
10 Chilungamo chanu sindinachibise mumtima mwanga.+Ndinalengeza za kukhulupirika kwanu ndi chipulumutso chanu.+Sindinabise kukoma mtima kwanu kosatha ndi choonadi chanu mumpingo waukulu.”+