Salimo 33:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Muimbireni nyimbo yatsopano.+Muimbireni choimbira cha zingwe ndi mtima wonse ndi kufuula mosangalala.+ Salimo 98:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 98 IMBIRANI Yehova nyimbo yatsopano,+Pakuti zimene wachita ndi zodabwitsa.+Dzanja lake lamanja, ndithu mkono wake woyera, wabweretsa chipulumutso.+ Salimo 113:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 113 Tamandani Ya, anthu inu!+Inu atumiki a Yehova, mutamandeni,+Tamandani dzina la Yehova.+
3 Muimbireni nyimbo yatsopano.+Muimbireni choimbira cha zingwe ndi mtima wonse ndi kufuula mosangalala.+
98 IMBIRANI Yehova nyimbo yatsopano,+Pakuti zimene wachita ndi zodabwitsa.+Dzanja lake lamanja, ndithu mkono wake woyera, wabweretsa chipulumutso.+